Danieli 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ataucotsa unyinjiwo udzakwezeka mtima wace; ndipo adzagwetsa zikwi makumi makumi, koma sadzalakika.

Danieli 11

Danieli 11:8-14