Cibvumbulutso 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo maonekedwe a dzombelo anafanana ndi akavalo okonzeka kukacita nkhondo; ndi pamitu pao ngati akorona onga agolidi, ndi pankhope pao ngati pankhope pa anthu.

Cibvumbulutso 9

Cibvumbulutso 9:5-17