Cibvumbulutso 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'masiku ajawo, anthu adzafunafuna imfa osaipeza konse; ndipo adzakhumba kumwalira, koma imfa idzawathawa.

Cibvumbulutso 9

Cibvumbulutso 9:1-13