Cibvumbulutso 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa Mwanawankhosa wakukhala pakati pa mpando wacifumu adzawaweta, nadzawatsogolera ku akasupe a madzi a moyo, ndipo Mulungu adzawapukutira misozi yonse pamaso pao.

Cibvumbulutso 7

Cibvumbulutso 7:9-17