Cibvumbulutso 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ndikupatsa ena oturuka m'sunagoge wa Satana akudzinenera okha ali Ayuda, osakhala Ayuda, komatu anama; taona, ndidzawadzetsa alambire pa mapazi ako, nazindikire kuti Ine ndakukonda.

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:5-18