Cibvumbulutso 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidziwa nchito zako (taona, ndapatsa pamaso pako khomo lotseguka limene munthu sakhoza kutsekapo), kuti uli nayo mphamvu pang'ono, ndipo unasunga mau anga, osakana dzina langa.

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:1-13