Cibvumbulutso 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye wakulakika, ndidzampatsa akhale pansi ndi Ine pa mpando wacifumu wanga, monga Inenso ndinalakika, ndipo ndinakhala pansi ndi Atate wanga pa mpando wacifumu wace.

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:18-22