Cibvumbulutso 3:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, ndaima pakhomo, ndigogoda; wina akamva mau anga nakatsegula pakhomo, ndidzalowa kwa iye, ndipo ndidzadya naye, ndi iye ndi Ine.

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:11-22