Cibvumbulutso 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapfuula ndi mau olimba, nanena, Wagwa, wagwa, Babulo waukuru, nusandulika mokhalamo ziwanda, ndi mosungiramo mizimu yonse yonyansa, ndi mosungiramo mbalame zonse zonyansa ndi zodanidwa.

Cibvumbulutso 18

Cibvumbulutso 18:1-7