Cibvumbulutso 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika m'Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukuru; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wace.

Cibvumbulutso 18

Cibvumbulutso 18:1-6