Cibvumbulutso 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panthawipo panali cibvomezi cacikuru, ndipo limodzi la magawo khumi a mudzi Iidagwa; ndipo anaphedwa m'cibvomezico anthu zikwi zisanu ndi ziwiri; ndipo otsalawo anakhala amantha, napatsa ulemerero kwa Mulungu wa m'Mwamba.

Cibvumbulutso 11

Cibvumbulutso 11:6-16