Cibvumbulutso 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamva mau akuru akucokera Kumwamba akunena nao, Kwerani kuno. Ndipo anakwera kumka Kumwamba mumtambo; ndipo adani ao anawapenya.

Cibvumbulutso 11

Cibvumbulutso 11:11-13