Cibvumbulutso 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene ndinamuona iye, ndinagwa pa mapazi ace ngati wakufa; ndipo anaika dzanja lace lamanja pa ine, nati, Usaope, ine ndine woyamba ndi wotsiriza,

Cibvumbulutso 1

Cibvumbulutso 1:8-18