Cibvumbulutso 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'dzanja lace lamanja munali nyenyezi zisanu ndi ziwirl; ndi m'kamwa mwace mudaturuka lupanga lakuthwa konse konse; ndipo nkhope yace ngati dzuwa lowala mu mphamvu yace.

Cibvumbulutso 1

Cibvumbulutso 1:10-20