Aroma 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti anawo asanabadwe, kapena asanacite kanthu kabwino kapena koipa, kuti kutsimikiza mtima kwa Mulungu monga mwa kusankha kukhale, si cifukwa ca nchito ai, koma cifukwa ca wakuitanayo,

Aroma 9

Aroma 9:7-15