Aroma 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma inu simuli m'thupi ai, koma mumzimu, ngatitu Mzimu wa Mulungu akhalabe mwa inu. Koma ngati munthu alibe Mzimu wa Kristu, siali wace wa Kristu.

Aroma 8

Aroma 8:5-13