Aroma 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati Kristu akhala mwa inu, thupilo ndithu liri lakufa cifukwa ca ucimo; koma mzimu uli wamoyo cifukwa ca cilungamo.

Aroma 8

Aroma 8:2-11