Aroma 8:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzatisiyanitsa ndani ndi cikondi ca Kristu? nsautso kodi, kapena kupsinjika mtima, kapena kuzunza, kapena njala, kapena usiwa, kapena zoopsya kapena lupanga kodi?

Aroma 8

Aroma 8:26-39