Aroma 8:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9 ndani adzawatsutsa? Kristu Yesu ndiye amene adafera, inde makamaka, ndiye amene adauka kwa akufa, 10 amene akhalanso pa dzanja lamanja la Mulungu, 11 amenenso atipempherera ife.

Aroma 8

Aroma 8:32-37