Aroma 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pamene anthu a mitundu akukhala opanda lamulo, amacita mwa okha za lamulo, omwewo angakhale alibe lamulo, adzikhalira okha ngati lamulo;

Aroma 2

Aroma 2:13-24