Aroma 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti anthu a mitundu yina akalemekeze Mulungu, cifukwa ca cifundo; monga kwalembedwa,Cifukwa ca icindidzakubvomerezani Inu pakati pa anthu amitundu,Ndidzayimbira dzina lanu.

Aroma 15

Aroma 15:1-19