Aroma 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinena kuti Kristu anakhala mtumiki wa mdulidwe, cifukwa ca coonadi ca Mulungu, kuti alimbikitse malonjezo opatsidwa kwa makolo,

Aroma 15

Aroma 15:1-17