Aroma 11:34-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Pakuti 5 anadziwitsa ndani mtima wace wa Ambuye? Kapena anakhala mphungu wace ndani?

35. Ndipo 6 anayamba ndani kumpatsa iye, ndipo adzambwezeranso?

36. Cifukwa 7 zinthu zonse zicokera kwa iye, zicitika mwa iye, ndi kufikira kwa iye. 8 K wa Iyeyo ukhale ulemerero ku nthawi zonse. Amen.

Aroma 11