Aroma 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa, Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera.

Aroma 12

Aroma 12:1-8