Aroma 11:29-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Pakuti 1 mphatso zace ndi kuitana kwace kwa Mulungu sizilapika.

30. Pakuti 2 monga inunso kale simunamvera Mulungu, koma tsopano mwalandira cifundo mwa kusamvera kwao,

31. coteronso iwo sanamvera tsopano, kuti iwonso akalandire cifundo, cifukwa ca cifundo ca kwa inu.

Aroma 11