Aroma 11:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo cotero Israyeli yense adzapulumuka; monganso kunalembedwa, kuti,Adzaturuka ku Ziyoni Mpulumutsi;Iye adzacotsa zamwano kwa Yakobo:

Aroma 11

Aroma 11:16-35