Aroma 11:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sindifuna, abale, kuti mukhale osadziwa cinsinsi ici, kuti mungadziyese anzeru mwa inu nokha, kuti kuuma mtima kunadza pang'ono pa Israyeli, kufikira kudzaza kwa anthu amitundu kunalowa;

Aroma 11

Aroma 11:19-34