Amosi 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzayendayenda peyupeyu kuyambira kunyanja kufikira kunyanja ndi kuyambira kumpoto kufikira kum'mawa; adzathamangathamanga kufunafuna mau a Yehova, koma osawapeza.

Amosi 8

Amosi 8:2-13