Amosi 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, akudza masiku, ati Ambuye Yehova, akuti ndidzatumiza njala m'dzikomo, si njala ya mkate kapena ludzu la madzi, koma njala ya kumva mau a Yehova.

Amosi 8

Amosi 8:4-14