Akolose 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndifuna kuti inu mudziwe nkhawa imene ndiri nayo cifukwa ca inu, ndi iwowa a m'Laodikaya, ndi onse amene sanaone nkhope yanga m'thupi;

Akolose 2

Akolose 2:1-5