Afilipi 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zimenenso mudaziphunzira, ndi kuzilandira, ndi kuzimva, ndi kuziona mwa ine, zomwezo citani; ndipo Mulungu wa mtendere adzakhala pamodzi ndi inu.

Afilipi 4

Afilipi 4:8-10