2 Timoteo 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma zindikira ici, kuti masiku otsiriza zidzafika nthawi zowawitsa.

2. Pakuti anthu adzakhala odzikonda okha, okonda ndarama, odzitamandira, odzikuza, amwano, osamvera akuwabala, osayamika,

2 Timoteo 3