2 Timoteo 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anthu adzakhala odzikonda okha, okonda ndarama, odzitamandira, odzikuza, amwano, osamvera akuwabala, osayamika,

2 Timoteo 3

2 Timoteo 3:1-12