2 Samueli 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali mnyamata wa m'nyumba ya Sauli dzina lace Ziba; ndipo anamuitana iye afike kwa Davide; ndi mfumuyo inanena naye, Iwe ndiwe Ziba kodi? Nati iye, Ndine mnyamata wanu ame.

2 Samueli 9

2 Samueli 9:1-5