2 Samueli 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anazindikira kuti Yehova anamkhazikitsa mfumu ya Israyeli, ndi kuti anakulitsa ufumu wace cifukwa ca anthu ace Israyeli.

2 Samueli 5

2 Samueli 5:5-18