2 Samueli 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hiramu mfumu ya Turo anatumiza mithenga kwa Davide ndi mitengo yamkungudza, ndi amisiri a matabwa, ndi omanga nyumba; iwo nammangira Davide nyumba.

2 Samueli 5

2 Samueli 5:6-16