2 Samueli 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Sauli, anamva kuti Abineri adakafera ku Hebroni, manja ace anafoka, ndi Aisrayeli onse anabvutika.

2 Samueli 4

2 Samueli 4:1-9