2 Samueli 3:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndikali wofoka ine lero, cinkana ndinadzozedwa mfumu; ndipo amuna awa ana a Zeruya andikakalira mtima; Yehova abwezere wocita coipa monga mwa coipa cace.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:34-39