2 Samueli 3:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manja anu sanamangidwa, mapazi anu sanalongedwa m'zigologolo;Monga munthu wakugwa ndi anthu oipa momwemo mudagwa inu.Ndipo anthu onse anamliranso.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:30-38