2 Samueli 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abineri analankhulanso m'kumva kwa Abenjamini; Abineri anamukanso ku Hebroni kulankhula m'makutu a Davide zonse zakukomera Aisrayeli ndi a nyumba yonse ya Benjamini.

2 Samueli 3

2 Samueli 3:17-22