2 Samueli 23:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zoonadi nyumba yanga siikhala yotere ndi Mulungu;Koma iye anapangana ndi ine pangano losatha,Lolongosoka mwa zonse ndi losungika;Pakuti ici ndi cipulumutso canga conse, ndi kufuma kwanga konse,Kodi sadzacimeretsa?

2 Samueli 23

2 Samueli 23:1-8