2 Samueli 20:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka namtsata anthu a Yoabu, ndi Akereti ndi Apeleti, ndi anthu onseamphamvu; naturuka m'Yerusalemu kukalondola Seba mwana wa Bikri.

2 Samueli 20

2 Samueli 20:1-17