2 Samueli 20:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inendine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika m'Israyeli; inu mulikufuna kuononga mudzi ndi mai wa m'Israyeli; mudzamezerang colowa ca Yehova?

2 Samueli 20

2 Samueli 20:10-22