2 Samueli 20:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkazi wanzeru wa m'mudzimo anapfuula, kuti, Imvani, imvani; munene kwa Yoabu, Bwerani pafupi kuno kuti ndgankhule nanu.

2 Samueli 20

2 Samueli 20:15-18