2 Samueli 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu Ayuda anabwera namdzoza Davide pomwepo akhale mfumu ya nyumba ya Yuda.Ndipo wina anauza Davide kuti, Anthu a ku Jabezi Gileadi ndiwo amene anamuika Sauli.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:1-11