2 Samueli 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anakwera nao anyamata ace okhala naye, munthu yense ndi banja lace; iwowa nakhala m'midzi ya Hebroni.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:1-13