2 Samueli 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abineri anabwereza kunena kwa Asaheli, Pambuka pakunditsata ine. Ndidzakukanthiranji kukugwetsa pansi? ndikatero ndidzaweramutsanso bwanji nkhope yanga kwa mbale wako Yoabu?

2 Samueli 2

2 Samueli 2:14-26