2 Samueli 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abineri ananena naye, Patuka iwe kulamanja kapena kulamanzere kwako nudzigwirire wina wa anyamatawo, nutenge zida zace. Koma Asaheli anakana kupambuka pakumtsata iye.

2 Samueli 2

2 Samueli 2:11-24