2 Samueli 18:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inanena ndi Mkusiyo, Mnyamatayo Abisalomu ali bwino? Mkusiyo nayankha, Adani a mbuye wanga mfumu, ndi onse akuukira inu kukucitirani zoipa, akhale monga mnyamata ujayo.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:30-33