2 Samueli 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, Mkusiyo anafika, nati, Mau akuuza mbuye wanga mfumu; pakuti Yehova anabwezera cilango lero onse akuukira inu.

2 Samueli 18

2 Samueli 18:28-33